1. Extract from Chichewa (Malawi) Test
Atate ake a Mumbi
nyemba |
Atate ake a Mumbi ndi mlimi. Ali ndi dimba lalikulu. Liri _________ ndi mudzi wawo. Matsiku onse __________ m'mawa ndi kupita kudimba kwao. Amalima __________, matimati ndi chimanga chambiri. Mumbi ___________ kudimba.
2. Extract from Nyanja (Zambia) Tests
Atate ace a Mumbi
nyemba |
Atate ace a Mumbi ndi mlimi. Ali ndi dimba lalikulu. Liri _________ ndi mudzi wawo. Matsiku onse ____________ m'mawa ndi kuyenda kudimba kwao. Amalima ___________, matimati ndi cimanga cambiri. Mumbi _____________ kudimba.